Maliko 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona Simoni ndi Andireya+ mchimwene wake wa Simoniyo, akuponya maukonde awo mʼnyanjamo+ chifukwa anali asodzi.+
16 Pamene ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona Simoni ndi Andireya+ mchimwene wake wa Simoniyo, akuponya maukonde awo mʼnyanjamo+ chifukwa anali asodzi.+