Maliko 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atapita patsogolo pangʼono, anaona Yakobo mwana wa Zebedayo ndi mchimwene wake Yohane, ali mungalawa yawo ndipo ankasoka maukonde awo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,8/1/2012, tsa. 18
19 Atapita patsogolo pangʼono, anaona Yakobo mwana wa Zebedayo ndi mchimwene wake Yohane, ali mungalawa yawo ndipo ankasoka maukonde awo.+