-
Maliko 1:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Nthawi yomweyo anawaitana. Choncho iwo anasiya bambo awo a Zebedayo mʼngalawamo limodzi ndi anthu aganyu ndipo anamutsatira.
-