Maliko 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Onsewo anachoka nʼkupita ku Kaperenao. Sabata litangoyamba, anakalowa musunagoge nʼkuyamba kuphunzitsa.+
21 Onsewo anachoka nʼkupita ku Kaperenao. Sabata litangoyamba, anakalowa musunagoge nʼkuyamba kuphunzitsa.+