Maliko 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mmenemo anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake, chifukwa ankawaphunzitsa monga munthu wokhala ndi ulamuliro, osati ngati alembi.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:22 “Wotsatira Wanga,” tsa. 101
22 Mmenemo anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake, chifukwa ankawaphunzitsa monga munthu wokhala ndi ulamuliro, osati ngati alembi.+