-
Maliko 1:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ataona zimenezi, anthu onse anadabwa kwambiri moti anayamba kukambirana kuti: “Kodi chimenechi nʼchiyani? Nʼchiphunzitso chatsopano! Ngakhale mizimu yonyansa akuilamula mwamphamvu ndipo ikumumvera.”
-