Maliko 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zitatero iwo anachoka kusunagogeko nʼkupita kunyumba kwa Simoni ndi Andireya. Yakobo ndi Yohane nawonso anapita nawo.+
29 Zitatero iwo anachoka kusunagogeko nʼkupita kunyumba kwa Simoni ndi Andireya. Yakobo ndi Yohane nawonso anapita nawo.+