Maliko 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho Yesu anachiritsa anthu ambiri amene ankadwala matenda osiyanasiyana+ ndipo anatulutsa ziwanda zambiri. Koma sanalole kuti ziwandazo zilankhule, chifukwa zinkamudziwa kuti ndi Khristu.*
34 Choncho Yesu anachiritsa anthu ambiri amene ankadwala matenda osiyanasiyana+ ndipo anatulutsa ziwanda zambiri. Koma sanalole kuti ziwandazo zilankhule, chifukwa zinkamudziwa kuti ndi Khristu.*