Maliko 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mʼmawa kwambiri kudakali mdima, Yesu anadzuka nʼkutuluka panja ndipo anapita kumalo kopanda anthu. Kumeneko anayamba kupemphera.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:35 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 9
35 Mʼmawa kwambiri kudakali mdima, Yesu anadzuka nʼkutuluka panja ndipo anapita kumalo kopanda anthu. Kumeneko anayamba kupemphera.+