Maliko 1:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi, koma upite ukadzionetse kwa wansembe ndipo chifukwa chakuti wayeretsedwa, ukapereke zinthu zimene Mose analamula,+ kuti ukhale umboni kwa iwo.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:44 Yesu—Ndi Njira, tsa. 65 Nsanja ya Olonda,2/15/2008, tsa. 284/15/1986, tsa. 9
44 Anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi, koma upite ukadzionetse kwa wansembe ndipo chifukwa chakuti wayeretsedwa, ukapereke zinthu zimene Mose analamula,+ kuti ukhale umboni kwa iwo.”+