45 Koma atachoka, munthu uja anayamba kulengeza zimenezo paliponse ndi kufalitsa nkhaniyo mʼmadera ena. Zimenezi zinachititsa kuti Yesu asathenso kulowa mumzinda uliwonse moonekera moti ankakhala kunja kopanda anthu. Koma anthu ankabwerabe kwa iye kuchokera kumbali zonse.+