-
Maliko 2:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma sakanatha kumufikitsa kwa Yesu chifukwa cha kuchuluka kwa anthu. Choncho anasasula denga pamene Yesu anali, ndipo ataboola padengapo, anatsitsirapo machira a munthu wakufa ziwalo uja.
-