Maliko 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Nʼchifukwa chiyani munthu ameneyu akulankhula chonchi? Akunyozatu Mulungu ameneyu. Ndi ndaninso wina amene angakhululukire machimo, si Mulungu yekha basi?”+
7 “Nʼchifukwa chiyani munthu ameneyu akulankhula chonchi? Akunyozatu Mulungu ameneyu. Ndi ndaninso wina amene angakhululukire machimo, si Mulungu yekha basi?”+