Maliko 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma nthawi yomweyo Yesu anazindikira mumtima mwake kuti iwo ankaganiza zimenezo, ndipo anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukuganiza zinthu zimenezi mʼmitima mwanu?+
8 Koma nthawi yomweyo Yesu anazindikira mumtima mwake kuti iwo ankaganiza zimenezo, ndipo anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukuganiza zinthu zimenezi mʼmitima mwanu?+