-
Maliko 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Chosavuta nʼchiti, kuuza wakufa ziwaloyu kuti, ‘Machimo ako akhululukidwa,’ kapena kunena kuti, ‘Nyamuka ndipo nyamula machira ako uyendeʼ?
-