Maliko 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Akudutsa anaona Levi mwana wa Alifeyo atakhala mu ofesi yokhomeramo msonkho ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Nthawi yomweyo ananyamuka nʼkumutsatira.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 68 Nsanja ya Olonda,5/15/1986, tsa. 8
14 Akudutsa anaona Levi mwana wa Alifeyo atakhala mu ofesi yokhomeramo msonkho ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Nthawi yomweyo ananyamuka nʼkumutsatira.+