Maliko 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nthawi inayake, ankadya chakudya* mʼnyumba mwa Levi ndipo anthu ambiri okhometsa msonkho komanso ochimwa ankadya limodzi ndi Yesu ndiponso ophunzira ake. Kumeneko kunali anthu ambiri amene ankamutsatira.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 68 Nsanja ya Olonda,5/15/1986, ptsa. 8-9
15 Nthawi inayake, ankadya chakudya* mʼnyumba mwa Levi ndipo anthu ambiri okhometsa msonkho komanso ochimwa ankadya limodzi ndi Yesu ndiponso ophunzira ake. Kumeneko kunali anthu ambiri amene ankamutsatira.+