-
Maliko 2:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma alembi a Afarisi, ataona kuti Yesu akudya limodzi ndi anthu ochimwa ndi okhometsa msonkho, anayamba kufunsa ophunzira ake kuti: “Bwanji akudya limodzi ndi okhometsa msonkho komanso anthu ochimwa?”
-