Maliko 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu atamva zimenezi anawayankha kuti: “Anthu amphamvu safunikira dokotala, koma odwala ndi amene amamufuna. Sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Yesu—Ndi Njira, tsa. 68 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, ptsa. 28-295/15/1986, tsa. 8
17 Yesu atamva zimenezi anawayankha kuti: “Anthu amphamvu safunikira dokotala, koma odwala ndi amene amamufuna. Sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”+