Maliko 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ophunzira a Yohane ndi Afarisi ankasala kudya. Choncho iwo anabwera kwa iye nʼkumufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ophunzira a Yohane ndi ophunzira a Afarisi amasala kudya, koma ophunzira anu sasala kudya?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:18 Yesu—Ndi Njira, tsa. 70 Nsanja ya Olonda,6/1/1986, ptsa. 8-9
18 Ophunzira a Yohane ndi Afarisi ankasala kudya. Choncho iwo anabwera kwa iye nʼkumufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ophunzira a Yohane ndi ophunzira a Afarisi amasala kudya, koma ophunzira anu sasala kudya?”+