Maliko 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anawayankha kuti: “Anzake a mkwati+ safunika kusala kudya ngati mkwatiyo ali nawo limodzi, si choncho kodi? Ngati mkwatiyo ali nawo limodzi sangasale kudya. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Yesu—Ndi Njira, tsa. 70 Nsanja ya Olonda,6/1/1986, tsa. 9
19 Yesu anawayankha kuti: “Anzake a mkwati+ safunika kusala kudya ngati mkwatiyo ali nawo limodzi, si choncho kodi? Ngati mkwatiyo ali nawo limodzi sangasale kudya.