Maliko 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Palibe amene amasokerera chigamba cha nsalu yatsopano pamalaya akunja akale. Akachita zimenezo, chigamba chatsopanocho chimakoka nʼkungʼamba malaya akalewo ndipo kungʼambikako kumawonjezereka kwambiri.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:21 Yesu—Ndi Njira, tsa. 70 Nsanja ya Olonda,6/1/1986, tsa. 9
21 Palibe amene amasokerera chigamba cha nsalu yatsopano pamalaya akunja akale. Akachita zimenezo, chigamba chatsopanocho chimakoka nʼkungʼamba malaya akalewo ndipo kungʼambikako kumawonjezereka kwambiri.+