-
Maliko 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndiponso, palibe munthu amene amathira vinyo watsopano mʼmatumba achikopa akale. Akachita zimenezo, vinyoyo amaphulitsa matumbawo. Kenako vinyoyo amatayika ndipo matumbawo amawonongeka. Koma anthu amathira vinyo watsopano mʼmatumba achikopa atsopano.”
-