Maliko 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ataona zimenezi Afarisiwo anatuluka ndipo nthawi yomweyo anapita kukakonza chiwembu limodzi ndi anthu amene ankatsatira Herode+ kuti amuphe. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,1/1/1987, tsa. 15
6 Ataona zimenezi Afarisiwo anatuluka ndipo nthawi yomweyo anapita kukakonza chiwembu limodzi ndi anthu amene ankatsatira Herode+ kuti amuphe.