Maliko 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yesu ndi ophunzira ake anachoka nʼkupita kunyanja ndipo chigulu cha anthu ochokera ku Galileya ndi ku Yudeya chinamutsatira.+
7 Koma Yesu ndi ophunzira ake anachoka nʼkupita kunyanja ndipo chigulu cha anthu ochokera ku Galileya ndi ku Yudeya chinamutsatira.+