-
Maliko 3:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndipo iye anauza ophunzira ake kuti amubweretsere ngalawa yaingʼono yoti akweremo kuti gulu la anthulo lisamupanikize.
-