Maliko 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza anali atachiritsa anthu ambiri, onse amene anali ndi matenda aakulu anamuunjirira kuti angomukhudza.+
10 Popeza anali atachiritsa anthu ambiri, onse amene anali ndi matenda aakulu anamuunjirira kuti angomukhudza.+