-
Maliko 3:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndiyeno anasankha gulu la anthu 12, amenenso anawapatsa dzina lakuti atumwi, kuti aziyenda naye nthawi zonse komanso kuti aziwatuma kukalalikira
-