-
Maliko 3:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Kunena zoona, palibe amene angalowe mʼnyumba ya munthu wamphamvu nʼkuba katundu wake ngati choyamba atapanda kumanga munthu wamphamvuyo. Akatero mʼpamene angathe kutenga katundu mʼnyumbamo.
-