Maliko 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano panafika mayi ake ndi azichimwene ake+ ndipo anaima panja nʼkutuma munthu kuti akamuitane.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:31 Kukambitsirana, tsa. 256
31 Tsopano panafika mayi ake ndi azichimwene ake+ ndipo anaima panja nʼkutuma munthu kuti akamuitane.+