Maliko 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Gulu la anthu linakhala momuzungulira ndipo anthuwo anamuuza kuti: “Mayi anu ndi azichimwene anu ali panjapa akukufunani.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:32 Kukambitsirana, tsa. 256
32 Gulu la anthu linakhala momuzungulira ndipo anthuwo anamuuza kuti: “Mayi anu ndi azichimwene anu ali panjapa akukufunani.”+