Maliko 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anawauza kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi woti mumvetse chinsinsi chopatulika+ cha Ufumu wa Mulungu. Koma amene ali kunja amauzidwa zonse pogwiritsa ntchito mafanizo+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Nsanja ya Olonda,2/15/2006, ptsa. 19-20
11 Iye anawauza kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi woti mumvetse chinsinsi chopatulika+ cha Ufumu wa Mulungu. Koma amene ali kunja amauzidwa zonse pogwiritsa ntchito mafanizo+