Maliko 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuti kuyangʼana, aziyangʼana ndithu koma asamaone. Kumva, azimva ndithu koma asamazindikire tanthauzo lake. Komanso kuti asatembenuke nʼkukhululukidwa.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:12 Nsanja ya Olonda,4/1/1987, tsa. 8
12 kuti kuyangʼana, aziyangʼana ndithu koma asamaone. Kumva, azimva ndithu koma asamazindikire tanthauzo lake. Komanso kuti asatembenuke nʼkukhululukidwa.”+