Maliko 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho mbewu zimene zimagwera mʼmbali mwa msewu ndi mawu amene afesedwa mwa anthu amene amati akangomva mawuwo, Satana amabwera+ nʼkudzachotsa mawu amene afesedwa mwa iwo.+
15 Choncho mbewu zimene zimagwera mʼmbali mwa msewu ndi mawu amene afesedwa mwa anthu amene amati akangomva mawuwo, Satana amabwera+ nʼkudzachotsa mawu amene afesedwa mwa iwo.+