Maliko 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mofanana ndi zimenezi, mbewu zimene zafesedwa pamiyala ndi mawu amene afesedwa mwa anthu omwe amati akangomva mawuwo, amawalandira mosangalala.+
16 Mofanana ndi zimenezi, mbewu zimene zafesedwa pamiyala ndi mawu amene afesedwa mwa anthu omwe amati akangomva mawuwo, amawalandira mosangalala.+