-
Maliko 4:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma iwo amakhala opanda mizu ndipo amapitirizabe kwakanthawi. Ndiyeno akangoyamba kuvutitsidwa kapena kuzunzidwa chifukwa cha mawuwo, amapunthwa.
-