Maliko 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 koma nkhawa za moyo+ wamʼnthawi* ino, chinyengo champhamvu cha chuma+ komanso kulakalaka zinthu+ zina zonse, zimalowa mʼmitima yawo nʼkulepheretsa mawuwo kukula ndipo sabereka zipatso. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:19 Galamukani!,11/2008, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 17
19 koma nkhawa za moyo+ wamʼnthawi* ino, chinyengo champhamvu cha chuma+ komanso kulakalaka zinthu+ zina zonse, zimalowa mʼmitima yawo nʼkulepheretsa mawuwo kukula ndipo sabereka zipatso.