Maliko 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anawauzanso kuti: “Nyale saivindikira ndi dengu* kapena kuiika pansi pa bedi, amatero ngati? Koma amaiika pachoikapo nyale,+ si choncho kodi? Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:21 Yesu—Ndi Njira, tsa. 110 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 184/1/1987, tsa. 8
21 Iye anawauzanso kuti: “Nyale saivindikira ndi dengu* kapena kuiika pansi pa bedi, amatero ngati? Koma amaiika pachoikapo nyale,+ si choncho kodi?