Maliko 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+
25 Chifukwa amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+