-
Maliko 4:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Munthuyo amagona usiku nʼkumadzuka kukacha ndipo mbewuzo zimamera nʼkukula. Koma mmene zimenezi zimachitikira, mwiniwakeyo sadziwa.
-