Maliko 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho atauza gulu la anthulo kuti lizipita, ophunzirawo anachoka naye pangalawa imene anakwera ija, koma analinso ndi ngalawa zina.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:36 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113 Nsanja ya Olonda,5/1/1987, tsa. 8
36 Choncho atauza gulu la anthulo kuti lizipita, ophunzirawo anachoka naye pangalawa imene anakwera ija, koma analinso ndi ngalawa zina.+