-
Maliko 4:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Koma Yesu anali kumbuyo kwa ngalawayo akugona, atatsamira pilo. Choncho anamudzutsa nʼkumufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi sizikukukhudzani kuti tikufa?”
-