Maliko 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma iwo anagwidwa ndi mantha aakulu ndipo anayamba kufunsana kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi ndani kwenikweni? Ngakhale mphepo ndi nyanja zikumumvera.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:41 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113 Nsanja ya Olonda,5/1/1987, tsa. 8
41 Koma iwo anagwidwa ndi mantha aakulu ndipo anayamba kufunsana kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi ndani kwenikweni? Ngakhale mphepo ndi nyanja zikumumvera.”+