Maliko 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo Yesu atangotsika mʼngalawa, anakumana ndi munthu wogwidwa ndi mzimu wonyansa akuchokera mʼmanda.* Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 114 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 65/15/1987, tsa. 26
2 Ndipo Yesu atangotsika mʼngalawa, anakumana ndi munthu wogwidwa ndi mzimu wonyansa akuchokera mʼmanda.*