-
Maliko 5:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Iye anamangidwapo ndi matangadza ndiponso maunyolo mobwerezabwereza, koma ankadula maunyolowo ndiponso kuthyola matangadzawo moti panalibe amene anatha kumugonjetsa.
-