Maliko 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ataona Yesu chapatali ndithu, anamuthamangira nʼkumugwadira.+