Maliko 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anafuula ndi mawu amphamvu kuti: “Kodi mukufuna chiyani kwa ine, Yesu, Mwana wa Mulungu Wamʼmwambamwamba? Ndikukulumbiritsani pali Mulungu kuti musandizunze.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:7 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 26
7 Kenako anafuula ndi mawu amphamvu kuti: “Kodi mukufuna chiyani kwa ine, Yesu, Mwana wa Mulungu Wamʼmwambamwamba? Ndikukulumbiritsani pali Mulungu kuti musandizunze.”+