Maliko 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho iye anailola. Atatero mizimu yonyansayo inatuluka nʼkukalowa munkhumbazo ndipo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi* nʼkulumphira mʼnyanja. Nkhumbazo zinalipo pafupifupi 2,000 ndipo zinamira mʼnyanjamo.
13 Choncho iye anailola. Atatero mizimu yonyansayo inatuluka nʼkukalowa munkhumbazo ndipo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi* nʼkulumphira mʼnyanja. Nkhumbazo zinalipo pafupifupi 2,000 ndipo zinamira mʼnyanjamo.