Maliko 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma abusa a ziwetozo anathawa nʼkukanena zimenezi mumzinda ndi mʼmidzi, ndipo anthu anabwera kudzaona zimene zinachitikazo.+
14 Koma abusa a ziwetozo anathawa nʼkukanena zimenezi mumzinda ndi mʼmidzi, ndipo anthu anabwera kudzaona zimene zinachitikazo.+