-
Maliko 5:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho anafika kwa Yesu ndipo anaona munthu amene anagwidwa ndi chiwanda uja, amene poyamba anali ndi gulu la mizimu yonyansa. Anamuona atakhala pansi, atavala bwinobwino komanso maganizo ake ali bwinobwino ndipo iwo anachita mantha.
-